Ho-yee mama wee! ah yeah
Ooh yeah aah mthefile
O! mama wee!
an*li kuti dzana, mtima utawawa
Nkhawa zitafika, anabwerera m'mbuyo
an*lira kosatha, usiku ndi usana
Atasweka mtima m'vuto lawo
Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru
Anayembekeza, amayankha
Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru
Anayembekeza, amayankha
Chorus
Anamuuza Yesu (Amayankha)
Anayitanirabe (Amayankha)
Dzina la Yehova (Amayamkha)
Zonse zinasintha (Amayankha)
Amayankha... yeah ihh
an*li kuti dzana, litavuta banja
Atakhumudwitsidwa misonzi ikutsika
Anadera nkhawa ntchito itasowa
Anavomereza kuti sadzayipeza
Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru
Anayembekeza poti amayankha
Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru
Anayembekeza ena nkumadabwa
Chorus
Anamuuza Yesu (Amayankha)
Anayitanirabe (Amayankha)
Dzina la Yehova (Amayamkha)
Zonse zinasintha (Amayankha)
Amayankha ah oh Amayankha
Bridge
Nanga ukulira chani iwe?
Pukuta misonzi
Zabwino zidzera oh, iwo oyembekeza, ooh uohuh!
Chorus til end