Chifundo Chikonga - Amayankha lyrics

Published

0 275 0

Chifundo Chikonga - Amayankha lyrics

Ho-yee mama wee! ah yeah Ooh yeah aah mthefile O! mama wee! an*li kuti dzana, mtima utawawa Nkhawa zitafika, anabwerera m'mbuyo an*lira kosatha, usiku ndi usana Atasweka mtima m'vuto lawo Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru Anayembekeza, amayankha Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru Anayembekeza, amayankha Chorus Anamuuza Yesu (Amayankha) Anayitanirabe (Amayankha) Dzina la Yehova (Amayamkha) Zonse zinasintha (Amayankha) Amayankha... yeah ihh an*li kuti dzana, litavuta banja Atakhumudwitsidwa misonzi ikutsika Anadera nkhawa ntchito itasowa Anavomereza kuti sadzayipeza Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru Anayembekeza poti amayankha Anamuuza Yesu, atathedwa nzeru Anayembekeza ena nkumadabwa Chorus Anamuuza Yesu (Amayankha) Anayitanirabe (Amayankha) Dzina la Yehova (Amayamkha) Zonse zinasintha (Amayankha) Amayankha ah oh Amayankha Bridge Nanga ukulira chani iwe? Pukuta misonzi Zabwino zidzera oh, iwo oyembekeza, ooh uohuh! Chorus til end

You need to sign in for commenting.
No comments yet.