Mwalandilidwa nonse, dsina langa ndine Esau Mwamwaya ndi Radioclit, The Very Best Tiyeni tonse tivine danse poti moto wayaka! Belita, Angela ndi Rita tabwera Joe, Jack ndi Mick tabwera Awiri! Awiri! Tivine limodzi Ponda! Ponda! Yalira ng'oma Kodi wawa, magaye, mwatani kodi mwakhala Khumakhuma Mwangotsamira mtengo M'maso muli penyapenya London iwe New York iwe Paris iwe Lilongwe iwe Ndati tikumbukenso mwa anzathu ena omwe Anatisiya kale, abale oimbawa anatisiya chabe M'mathupi, koma nyimbo zawo zizakhala zikumueka Mpakana kalekale Fumulani iwe Gwilani iwe Bob Marley iwe Matafale iwe