The Very Best - Warm heart of africa lyrics

Published

0 104 0

The Very Best - Warm heart of africa lyrics

Is hip-hop hereditary? I don't know Oh, the boys move fast You should take it slow Well, we all need someone to tell us when to go A beat-box imaginary in the show All you shell-toes lined up in a row All your favorite breaks Your favorite ELO Musadabwe ndikamavina ine gule wakwathu uuuu Kum'mwera kwa Africa kule dziko limodzi lotchedwa Malawi iiii Warm heart of Africa kuli magule magule okoma aaaa Tchopa, manganje, ngoma, vimbuza, maseche ndi M'ganda aaaa Zikomo zikomo nonse Kodi muli bwanji Ine ndili bwino ooooo Alendo asaononge Dziko la mtendere Malawi wabwino ooooo Zikatere zikatere tiyeni tilowe m'bwalo Zikatere zikatere wayaka moto oo Zikatere zikatere pali ngozi pano Zikatere zikatere malawi moto oo Oh please tell me when to go Iwe newo

You need to sign in for commenting.
No comments yet.