Published 2016-11-05
0 134 0
Ukakhala iwe mphwanga Usadzinamize uli ndi abale Amakukonda uli ndi chuma Ukasauka kukutaya Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi Umawundana kuposa madzi Iwe iwe mvera Tchera tchera khutu Ganiza ngati munthu
You need to sign in for annotating