Revolver - Ndiwe Number One lyrics

Published

0 124 0

Revolver - Ndiwe Number One lyrics

[Chorus-Sir Patricks] Chikondi ndichophweka ukapeza soul mate Uzakhala wokoma moyo wako wonse Ukazapeza namwali wachikondi ngati wangadi Ngati wangadi yeah Ndiwe number one (poti sukudziwa) Ndiwe number one (uleke kulota) Ndiwe number one (poti sukudziwa) Ndiwe number one ndimawelengela [verse 1-Revolver] One, ndiwe one ngati Mata Okuposa palibe iwe, ata Olo zinthu zitavuta bwanji ndikakhala ndiwe m'mtima mumakhala bata Two, ena kutokota timagontha nkhutu Its just us two Zima looks tho Siwe nkhwangwa, no Koma umandiwazatu Dont you ever forget You all that i need, no Meth Nthawi zonse dzina langa limakhala mkamwa mwa anthu ngati colgate Ndinkakhala ndi uyu lero mawa ndi wina But you is a keeper ngati Pepe Reina This feeling is new to me Tabwela ndikuwuze what you do to me (back to chorus) [verse 2-Revolver] You blow me away you the bomb bae Uli hot ngati phwanya yaku bombay I can look in those eyes all day Game ndimaisata but i dont play Ndinali player koma pano ndinabinya ah Wofuna kulanda zimudinya ah Mwini wake wa mtima wanga iwe Umawala mu mdima wanga iwe You see i dont love you coz i need you, i need you coz i love you Olo nditaluza chili chonse i can still get through it as long as i have you My love ain't blind Imawona but it just dont mind Eh ili sisewelo Iwe wekha nzakuveka velo (back to chorus 2x)

You need to sign in for commenting.
No comments yet.