Kumsokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa Kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako Mwana apate eti tiona ngati agone Kumsokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa Kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako Mwana apate eti tiona ngati agone Chaka chino chokha iye akagonera kumanda M'mati n'kwere ndakwera panyumba yanthakati Wakoma bana pawaka Wamara bana nsokoto Mwana akangoti agone
Kum'bwerera usiku Thupi lonse lamangika Kulephera kufuula Poti adsuke mam'mawa Thupi kunjenjemera Mutu wanga, malungo, matenda aja akula Wakoma bana Wati kitasha Wamara bana Ichi n'chasoni Nsokoto nsokoto Nsokoto nsokoto Muuze nthakatiyo namulondola ife takana Bana bakunsokoto ise Bana bakumulowe ise Bana bamwakisulu ise Bana bakaronga ise Bana bakurumphi ise Bana bakuchitipa ise