Verse 1(Chavura) Mu b town ndimafila life (LIFE) Aliyense oyimba ndi ine ndimak**er guys (GUYS) Ndikamalemba verse ndimatcheka line up (UP) Kuyisiya fans m'madzi ngati pine appl' Ndimazisata amathoka sh** (sh*t) Amasata nkhani zanga ndikasoka chick (CHICK) Mafanawa pa internet amandistokadi Akandipeza amandifunsa, amandibowadi Zowonadinso mafanawa simachita show (SHOW) Ronald'nso nyimbo zawo samamixer bho (BHO) Tawonaninso achina volver amangoakhilanso Amafuna atandibula ngati filabo Pozandibula azafila bho (BHO) Ngati chick yopanda mbina sazachithako(KO) Chino ndichiakita mfana sazachiphako(KO) Wake ndadya koma wanga sazachi... ha Chorus(Stich fray) (Kuyenda ntown) aliyense maso pa ine,amene samandiziwa angoti uje bwanji (Ndiyende ntown) aliyense maso pa ine,amene samandidziwa angoti uje bwanji Amene amandiziwa akuti ndine DOLO Amene amandiziwa akuti ndine SHASHA Amene amandiziwa akuti ndine DOLO Amandifila fukwa ndine waku blantyre Verse 2(Revolver) Akuti volver timakufila ku mponela
Nyimbo zanyuwanizo muzitiponyela Achina mbina mbina muziti ponyela Ndikutentha mahater sakuwothela Amanditcha austin, mfana wa powers Osati movie, ndikuthoka za bawazi Green ndimamwa, mu tracks ndimamudya Akuti ndi mfumu komabe ndimamuda Get it, musamude fumu-lani Stich andifunsa 'iwe volver uku-tani Zomapanga beef suzatukuka nazo Olo utahitter sakutenga kuma show' Neighbour wanga akuboweka Sandiziwa koma nyimbo zanga akuloweza Speakers on blast, chifisi pa repeat Ine nditachokapo kubwela round six (chorus) Verse 3 (Stich fray) yeah,them wan fi follow me ina real life But mi so tweeter me forget & mi nah follow back Amati hater koma chonsecho amatifila Ngati ma chick awo athetsa amatilira Check it afuna khalangati ifedi, Kuzimva u landlord mu gameyi koma ali pa rent (HA HA HA HA) , ndima students ozimva u head, Ratatatatatata,stichfray ndinedi Ndinedi DOLO Amene amandiziwa akuti ndine SHASHA Amene amandiziwa akuti ndine DOLO Mukut sim'mandiziwa pamene ndimakubowani (chorus 2x)